Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:
1. N’cifukwa ciani tiyenela kulimbitsa cikhulupililo cathu pali pano? (Aheb. 10:39)
2. Kodi ‘tingamuone’ bwanji Yehova ngakhale kuti ni wosaoneka? (Aheb. 11:27)
3. N’cifukwa ciani kupenda maulosi a m’Baibo n’kopindulitsa? (Aroma 10:17)
4. Kodi mzimu woyela ungatithandize bwanji kukhala na cikhulupililo? (Luka 11:13; Agal. 5:22)
5. Kodi tingaŵathandize bwanji ena kulimbitsa cikhulupililo cawo? (1 Ates. 2:7, 8)
6. N’cifukwa ciani tiyenela ‘kuyang’anitsitsa Mtumiki Wamkulu ndi Wokwanilitsa cikhulupililo cathu’? (Aheb. 12:2, 3)
© 2021 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CA-brpgm22-CIN