Tsiku Loyamba
“Tiwonjezeleni cikhulupililo”—Luka 17:5
M’MAŴA
9:20 Vidiyo ya Nyimbo
9:30 Nyimbo Na. 5 na Pemphelo
9:40 NKHANI YA CHEYAMANI: Kodi Cikhulupililo N’camphamvu Motani? (Mateyu 17:19, 20; Aheberi 11:1)
10:10 YOSIYILANA: Cifukwa Cake Timakhulupilila . . .
• Kuti Mulungu Aliko (Aefeso 2:1, 12; Aheberi 11:3)
• Mawu a Mulungu (Yesaya 46:10)
• Miyezo ya Mulungu ya Makhalidwe Abwino (Yesaya 48:17)
• Cikondi ca Mulungu (Yohane 6:44)
11:05 Nyimbo Na. 37 na Zilengezo
11:15 KUŴELENGA BAIBO MONGA SEŴELO: Nowa—Cikhulupililo Cinamusonkhezela Kumvela Mulungu (Genesis 6:1–8:22; 9:8-16)
11:45 ‘Khalani ndi Cikhulupililo, Osakayika’ (Mateyu 21:21, 22)
12:15 Nyimbo Na. 118 na Kupumula
MASANA
13:35 Vidiyo ya Nyimbo
13:45 Nyimbo Na. 2
13:50 YOSIYILANA: Yang’anani Cilengedwe Kuti Mulimbitse Cikhulupililo Canu
• Nyenyezi (Yesaya 40:26)
• Nyanja Zamcele (Salimo 93:4)
• Nkhalango (Salimo 37:10, 11, 29)
• Mphepo na Madzi (Salimo 147:17, 18)
• Zolengedwa za m’Nyanja (Salimo 104:27, 28)
• Matupi Athu (Yesaya 33:24)
14:50 Nyimbo Na. 148 na Zilengezo
15:00 Nchito Zamphamvu za Yehova Zimalimbitsa Cikhulupililo (Yesaya 43:10; Aheberi 11:32-35)
15:20 YOSIYILANA: Tengelani Citsanzo ca Anthu a Cikhulupililo, Osati Opanda Cikhulupililo
• Abele, Osati Kaini (Aheberi 11:4)
• Inoki, Osati Lameki (Aheberi 11:5)
• Nowa, Osati Anthu a m’Nthawi Yake (Aheberi 11:7)
• Mose, Osati Farao (Aheberi 11:24-26)
• Ophunzila a Yesu, Osati Afarisi (Machitidwe 5:29)
16:15 “Pitilizani Kudziyesa Kuti Muone Ngati Mukadali Olimba m’Cikhulupililo”—Motani? (2 Akorinto 13:5, 11)
16:50 Nyimbo Na. 119 na Pemphelo