Tsiku Loyamba
“Yehova adzadalitsa anthu ake ndi mtendele.”—Salimo 29:11
M’maŵa
8:20 Vidiyo ya Nyimbo
8:30 Nyimbo Na. 86 na Pemphelo
8:40 NKHANI YA CHEYAMANI: Yehova ni “Mulungu Amene Amapatsa Mtendele” (Aroma 15:33; Afilipi 4:6, 7)
9:10 YOSIYILANA: Mmene Cikondi Cimabweletsela Mtendele Weniweni
• Kukonda Mulungu (Mateyu 22:37, 38; Aroma 12:17-19)
• Kukonda Anansi Athu (Mateyu 22:39; Aroma 13:8-10)
• Kukonda Mawu a Mulungu (Salimo 119:165, 167, 168)
10:05 Nyimbo Na. 24 na Zilengezo
10:15 KUŴELENGA BAIBO MONGA SEŴELO: Yakobo—Munthu Wokonda Mtendele (Genesis 26:12–33:11)
10:45 “Nchito ya Cilungamo Ceniceni Idzakhala Mtendele” (Yesaya 32:17; 60:21, 22)
11:15 Nyimbo Na. 97 na Kupumula
Masana
12:35 Vidiyo ya Nyimbo
12:45 Nyimbo Na. 144
12:50 YOSIYILANA: Kondwelani na Malonjezo a Mulungu Okamba za Mtendele
• “Atumiki Anga Adzadya . . . Atumiki Anga Adzamwa” (Yesaya 65:13, 14)
• “Iwo Adzamanga Nyumba n’Kukhalamo,” Ndipo “Adzabzala Minda ya Mpesa.” (Yesaya 65:21-23)
• “Mmbulu ndi Mwana wa Nkhosa Zidzadyela Pamodzi” (Yesaya 11:6-9; 65:25)
• “Palibe Munthu Wokhala m’Dzikolo Amene Adzanene Kuti: ‘Ndikudwala’” (Yesaya 33:24; 35:5, 6)
• “Iye Adzameza Imfa Kwamuyaya” (Yesaya 25:7, 8)
13:50 Nyimbo Na. 35 na Zilengezo
14:00 YOSIYILANA: Zofunikila Kuti M’banja Mukhale Mtendele
• Kuonetsana Cikondi na Ulemu (Aroma 12:10)
• Kukambilana Momasuka (Aefeso 5:15, 16)
• Kucita Zinthu Monga Timu (Mateyu 19:6)
• Kulambila Yehova Capamodzi (Yoswa 24:15)
14:55 Thandizilani “Kalonga Wamtendele” Mokhulupilika (Yesaya 9:6, 7; Tito 3:1, 2)
15:15 Musasoceletsedwe na Mtendele Wabodza! (Mateyu 4:1-11; Yohane 14:27; 1 Atesalonika 5:2, 3)
15:50 Nyimbo Na. 112 na Pemphelo Lothela