LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 156
  • Mwa Cikhulupililo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mwa Cikhulupililo
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tikhale na Cikhulupililo
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • “Tionjezeleni Cikhulupililo”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Tikhale ndi Chikhulupiriro
    Imbirani Yehova
  • Khalani na Cikhulupililo m’Malonjezo a Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 156

NYIMBO 156

Mwa Cikhulupililo

Yopulinta

(Salimo 27:13)

  1. 1. Sinidzayopa mkango.

    Sinidzayopa imfa.

    Yehova ali nane

    olo nivutike.

    Yehova sanganisiye.

    (KOLASI)

    Nidzayenda

    mwa cikhulupililo.

    Palibenso

    cidzanifo’ketsa.

    Sinidzacita mantha.

    Nidzalimba mtima.

    M’lungu wanga

    sanganisiye.

    Sin’dzayopa.

  2. 2. Atumiki akale

    Okhulupilikawo

    Anapililabe;

    adzaukitsidwa.

    Ndipo onse adzaona.

    (KOLASI)

    Nidzayenda

    mwa cikhulupililo.

    Palibenso

    cidzanifo’ketsa.

    Sinidzacita mantha.

    Nidzalimba mtima.

    M’lungu wanga

    sanganisiye.

    Sin’dzayopa.

    (BILIJI)

    Nimadziŵa

    ciyembekezoci

    Cidzanilimbitsa

    mtima.

    N’dzapilila

    mayeselo

    na mavuto,

    Ndipodi sinidzafo’ka.

  3. 3. Niona madalitso

    Ali m’tsogolomu.

    N’dzalimbikila

    Cifukwa nidziŵa

    kuti Yehova ’dzapambana.

    (KOLASI)

    Nidzayenda

    mwa cikhulupililo.

    Palibenso

    cidzanifo’ketsa.

    Sinidzacita mantha.

    Nidzalimba mtima.

    M’lungu wanga

    sanganisiye.

    Sin’dzayopa.

    Sin’dzayopa.

(Onaninso Aheb. 11:1-40.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani