‘Siticita Manyazi na Uthenga Wabwino’
M’maŵa
8:40 Nyimbo Zamalimba
8:50 Nyimbo Na. 67 na Pemphelo
9:00 N’cifukwa Ciyani Siticita Nawo Manyazi Uthenga Wabwino?
9:15 Kukhalila Kumbuyo Uthenga Wabwino
9:30 Khalani “Munthu Wosacita Manyazi ndi Nchito Imene Wagwila”
9:55 Nyimbo Na. 73 na Zilengezo
10:05 Onetsani Mzimu Wamphamvu, Wacikondi, Komanso Woganiza Bwino
10:35 Ubatizo: Pitilizani ‘Kugonjela Uthenga Wabwino’
11:05 Nyimbo Na. 75
Masana
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 77
12:35 Zocitika
12:45 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:15 Nkhani Yosiyilana: Siticita Nawo Manyazi . . .
• Malamulo a Mulungu
• Ufumu wa Mulungu
• Anthu Oimilako Mulungu
14:00 Nyimbo Na. 40 na Zilengezo
14:10 ‘Dzitamandileni mwa Yehova’
14:55 Nyimbo Na. 7 na Pemphelo