“Makhalidwe Anu Akhale Ogwilizana ndi Uthenga Wabwino”
AFILIPI 1:27
Mmawa
8:40 Nyimbo Zamalimba
8:50 Nyimbo Na. 35 na Pemphelo
9:00 Kodi Uthenga Wabwino Ukukusinthani Motani?
9:15 Yosiyilana: Mmene Uthenga Wabwino Unakhudzila Umoyo Wawo
• Sitefano
• Filipo
• Akula na Purisikila
• Tito
10:05 Nyimbo Na. 76 na Zilengezo
10:15 Pitilizani Kukhala “Odzipeleka kwa Mulungu”
10:35 Ubatizo: Pitilizani ‘Kugonjela Uthenga Wabwino’
11:05 Nyimbo Na. 37
Masana
12:20 Nyimbo Zamalimba
12:30 Nyimbo Na. 56 na Pemphelo
12:35 Nkhani ya Anthu Onse: N’ciyani Cimakupangitsani Kukhulupilila Zimene Mumakhulupilila?
13:05 Cidule ca Nsanja ya Mlonda
13:35 Nyimbo Na. 24 na Zilengezo
13:45 Yosiyilana: “Tikusonyeza. . . Kuti Ndife Atumiki a Mulungu . . . ”
• Popilila
• Pokhala Okoma Mtima
• Pokhala Oona Mtima
14:30 Kodi Mukuphunzitsidwa Motani?
15:00 Nyimbo Na. 29 na Pemphelo