Pezani Mayankho pa Mafunso Aya:
1. Tingaonetse motani kuti ‘timamvera zimene mzimu ukunena’? (Chiv. 1:3, 10, 11; 3:19)
2. N’ciyani cingatithandize kupitiriza kugwira nchito mwakhama komanso kupirira? (Chiv. 2:4)
3. Kodi tingacite ciani kuti tikonzekere kupirira cizunzo molimba mtima? (Miy. 29:25; Chiv. 2:10, 11)
4. Kodi tingacite ciani kuti tipewe kukana kuti timakhulupirira Yesu? (Chiv. 2:12-16)
5. Kodi tingacite ciani kuti tipitirize kugwira mwamphamvu zinthu zimene tiri nazo? (Chiv. 2:24, 25; 3:1-3, 7, 8, 10, 11)
6. N’ciani cingatithandize kukhalabe odzipereka? (Chiv. 3:14-19; Mat. 6:25-27, 31-33)
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
CA-brpgm26-CIN