1914-2014 Ufumu Wakhala Ukulamulila Kwa Zaka 100
Mu 1922, m’bale J.F. Rutherford analengeza molimba mtima kuti: “Onani, Mfumu yayamba kale kulamulila . . . Lengezani Mfumu ndi ufumu wake.” Caka cino, Ufumu wakwanitsa zaka 100 ukulamulila ndipo cilengezo cimeneco cimaticititsa cidwi mpaka pano. Kuti mwezi wa August ukhale wapadela kwambili, tiyeni tonse ticite khama kuthandiza anthu kudziŵa za Ufumu wa Mulungu pogwilitsila nchito Webu saiti yathu.