LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 April tsa. 2
  • Mbali Yatsopano Yoyambitsila Makambilano

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mbali Yatsopano Yoyambitsila Makambilano
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • MMENE TINGASEŴENZETSELE MBALI IMENEYI:
  • Mmene Tingayambitsile Makambilano Pogwilitsila Nchito Mathirakiti
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Kambilanani Nkhani Imodzi, Koma Gaŵilani Magazini Onse Aŵili
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Tumapepala Twauthenga Twatsopano Topangidwa Mosangalatsa!
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Gwilitsilani Nchito “Mfundo za m’Mau a Mulungu”—Poyambitsa Makambilano
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 April tsa. 2

UMOYO WATHU WACIKRISTU

Mbali Yatsopano Yoyambitsila Makambilano

Duwa pamanda

Kuyambila ndi Nsanja ya Mlonda yogaŵila ya Na. 1 2016, patsamba lothela pakhala pakupezeka mbali yakuti “Kodi Baibulo Limakamba Ciani?” Mbali yatsopano imeneyi yakonzedwa kuti itithandize kuyamba kukambilana ndi anthu nkhani za m’Baibulo. Mbaliyi yakonzedwa mofanana ndi tumapepala twauthenga. Pali funso ndi yankho la m’Malemba, komanso mfundo zina zofunika kukambilana.

Makambilano osangalatsa ozikidwa pa nkhani za m’malemba, amatithandiza kuyambitsa maphunzilo a Baibulo. Seŵenzetsani mbali imeneyi pothandiza anthu kuthetsa njala yao ya kuuzimu.—Mat. 5:6.

MMENE TINGASEŴENZETSELE MBALI IMENEYI:

  1. Funsani mwininyumba funso limodzi pa mafunso amene alipo

  2. Mvetselani mosamala ndipo muyamikileni pa yankho lake

  3. Ŵelengani lemba limene lili pa kamutu kakuti, “Zimene Baibulo Limakamba,” ndipo m’funseni maganizo ake pa vesi limenelo. Ngati ali ndi nthawi, pitilizani kukambilana mfundo imene ili pa kamutu kakuti “Zina Zimene Baibulo Limakamba.”

  4. Gaŵilani magazini

  5. Pangani makonzedwe akuti mukabweleleko kudzakambilana funso laciŵili

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani