LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 August tsa. 1
  • Maulaliki a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • GALAMUKANI!
  • GALAMUKANI!
  • MVETSELANI KWA MULUNGU KUTI MUKHALE NDI MOYO WAMUYAYA
  • KONZANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 August tsa. 1
Mwamuna ndi mkazi wake aseŵenzetsa intakomu polalikila ku Vienna, m’dziko la Austria

Aseŵenzetsa intakomu polalikila ku Vienna, m’dziko la Austria

Maulaliki a Citsanzo

GALAMUKANI!

Galamukani! Na. 4 | Kodi N’zotheka Kusintha Zomwe Munazolowera?

Funso: Kodi muganiza kuti munthu angapindule bwanji ngati ayesetsa kuleka zizoloŵezi zoipa?

Lemba: Mlal. 7:8a

Cogaŵila: Nkhani izi zifotokoza mfundo za m’Baibulo zimene zingathandize anthu kusintha zizoloŵezi zawo kuti akhale na umoyo wabwino.

GALAMUKANI!

Funso: Zinthu pa umoyo zimasintha-sintha. Muganiza kuti n’ciani cingatithandize kukhalabe acimwemwe ngati zinthu zina zasintha pa umoyo wathu?

Lemba: Mlal. 7:10

Cogaŵila: [Aonetseni nkhani imene iyambila patsamba 10.] Nkhani iyi ifotokoza mfundo za m’Baibulo zimene zingatithandize ngati zinthu zina zasintha pa umoyo wathu.

MVETSELANI KWA MULUNGU KUTI MUKHALE NDI MOYO WAMUYAYA

Mvetselani kwa Mulungu Kuti Mukhale ndi Moyo Wamuyaya

Funso: Aliyense wa ife ali na dzina. Ngakhale acibale athu ndi anzathu naonso ali na maina. Nanga Mulungu dzina lake n’ndani?

Lemba: Sal. 83:18

Cogaŵila: Kabuku aka kafotokoza zinthu zina zambili zimene Baibulo imakamba ponena za Mulungu. [Afotokozeleni mwacidule zimene zili pa masamba 6 ndi 7.]

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani