LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 April tsa. 1
  • Maulaliki a Citsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Maulaliki a Citsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • GALAMUKANI!
  • PHUNZITSANI COONADI
  • KODI UFUMU WA MULUNGU N’CIANI? (Ulendo Wobwelelako)
  • KONZANI ULALIKI WANU
  • Maulaliki a Citsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Maulaliki Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 April tsa. 1
Mlongo wozilala akulandilidwa bwino ndi mpingo

Alandila mlongo amene wayambanso kubwela ku Nyumba ya Ufumu

Maulaliki a Citsanzo

GALAMUKANI!

Galamukani! Na. 2 2017 | N’ciani cili kuseli kwa zamizimu?

Funso: Masiku ano, m’mafilimu ambili na mapulugilamu a pa TV amatambitsa mfiti, viŵanda, vipuku ndi zina zotelo. Kodi imwe m’maziona bwanji? Kodi n’zosangalatsa cabe zopanda vuto lililonse, kapena pali ziopsezo zinazake?

Cogaŵila: Galamukani! iyi ifotokoza cifukwa cake anthu amacita cidwi kwambili ndi zinthu zamizimu. Ifotokozanso cimene cili kuseli kwa zinthu zimenezi.

PHUNZITSANI COONADI

Baibo yotsegula

Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu udzathetsa bwanji mavuto padziko?

Lemba: Mat. 6:10

Mfundo ya Coonadi: Ufumu wa Mulungu udzabweletsa mgwilizano, bata na mtendele padziko lapansi, monga mmene unacitila kale kumwamba.

KODI UFUMU WA MULUNGU N’CIANI? (Ulendo Wobwelelako)

Kodi Ufumu wa Mulungu N’ciani?

Funso: [Muonetseni funso lili kumbuyo kwa kapepa.] Kodi moyo udzakhala wotani mu Ufumu wa Mulungu?

Malemba: Sal. 37:29; Yes. 65:21-23

Cogaŵila: [Muonetseni kabuku ka Uthenga Wabwino] Phunzilo 7 m’kabukuka ifotokoza mmene malonjezo amenewa angapindulitsile imwe na ine. [Yambitsani phunzilo la Baibo ndi kabukuka.]

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila:

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani