CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YEREMIYA 32-34
Cizindikilo Cakuti Isiraeli Adzabwezeletsedwa
Yopulinta
32:9-14
Yeremiya anatsatila ndondomeko pogula munda
33:10, 11
Yehova anaonetsa ubwino wake mwa kulonjeza kuti otengeledwa ku ukapolo amene anamvela malangizo ake adzawakhululukila na kuwabweza ku Isiraeli