CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EZEKIELI 18-20
Kodi Yehova Akatikhululukila Macimo, Amawakumbukilanso?
18:21, 22
Yehova akatikhululukila macimo, samadzatiimbanso mlandu cifukwa ca macimowo.
Zitsanzo za anthu a m’Baibo zimatithandiza kukhulupilila kuti Yehova amatikhululukiladi.
Mfumu Davide
N’ciani cimene analakwa?
N’cifukwa ciani anam’khululukila?
Kodi Yehova anamuonetsa bwanji kuti anam’khululukila?
Mfumu Manase
N’ciani cimene analakwa?
N’cifukwa ciani anam’khululukila?
Kodi Yehova anamuonetsa bwanji kuti anam’khululukila?
Mtumwi Petulo
N’ciani cimene analakwa?
N’cifukwa ciani anam’khululukila?
Kodi Yehova anamuonetsa bwanji kuti anam’khululukila?