LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • wp20 na. 3 tsa. 16
  • Kodi Munadzifunsapo?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Munadzifunsapo?
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambili Onena za Umoyo?
    Tingapeze Kuti Mayankho a Mafunso Ofunika Kwambili Onena za Umoyo?
  • Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?
    Kodi Zinthu Zidzakhala Bwanji Mtsogolo?
  • Kodi Baibo Mumaiona Bwanji?
    Kodi Baibo Mumaiona Bwanji?
  • Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?
    Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yogawila)—2020
wp20 na. 3 tsa. 16

Kodi Munadzifunsapo?

  • Foni ili pafupi na makapu aŵili a khofi. Ndipo kabuku kakuti ‘Real Faith—Your Key to a Happy Life’ kaonekela pa foni imeneyo.

    N’cifukwa ciani padzikoli pali mavuto ambili?

  • Kodi mungacite ciani kuti mupeze nzelu zokuthandizani kupilila mavuto mu umoyo?

  • Kodi Mulungu amasamala za imwe?—1 Petulo 5: 6, 7.

  • Kodi mungacite ciani kuti mudziŵe zambili za Mulungu komanso cifunilo cake?

Anthu ofika mamiliyoni apeza mayankho okhutilitsa pa mafunso amenewa, mwa kuŵelenga Malemba Oyela. Na imwe mungawapeze mayankho.

Ngati mufuna kudziŵa zambili, conde pemphani kabuku kakuti Real Faith—Your Key to a Happy Life, kwa ofalitsa magazini ino ndipo adzakutumizilani mahala, kapena mungakaŵelenge pa intaneti pa www.jw.org.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani