CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | LUKA 14-16
Fanizo la Mwana Woloŵelela
Zimene tiphunzilapo pa fanizo ili.
Cimakhala canzelu kukhalabe m’gulu lotetezeka la anthu a Mulungu, limene Atate wathu wacikondi akulisamalila
Tikapatuka pa njila ya Yehova, modzicepetsa tiyenela kubwelelanso tili na cidalilo cakuti Yehova adzatikhululukila
Tingatengele citsanzo ca Yehova mwa kulandila na manja aŵili anthu amene alapa na kubwelelela mu mpingo