CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | LUKA 23-24
Muzikhala Okonzeka Kukhululukila Ena
Kodi nikhululukile ndani?
Kodi kukhala “wokonzeka kukhululuka” kumatanthauza ciani? (Sal. 86:5) Yehova na Mwana wake amafufuza kuti aone ngati anthu amene acimwa ali na mtima wolapa n’colinga cakuti awacitile cifundo.