Amanga Nyumba ya Ufumu ku Australia
Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi tingapeze kuti citonthozo tikafeledwa?
Lemba: 2 Akor. 1:3, 4
Ulalo: N’ciani cimacitika munthu akamwalila?
○●○ KUBWELELAKO KOYAMBA
Funso: N’ciani cimacitika munthu akamwalila?
Lemba: Mlal. 9:5, 10
Ulalo: Kodi tili na ciyembekezo canji cokhudza akufa?
○●○ KUBWELELAKO KACIŴILI
Funso: Kodi tili na ciyembekezo canji cokhudza akufa?
Lemba: Mac. 24:15
Ulalo: Kodi anthu akufa adzaukila kuti?