Akugwila nchito yothandiza anthu amene akumana na tsoka la zacilengedwe ku United States
Makambilano Acitsanzo
●○○ULENDO WOYAMBA
Funso: N’ciani cimacitika munthu akamwalila?
Lemba: Mlal. 9:5a
Ulalo: Kodi imfa ni mapeto a zonse?
○●○ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
Funso: Kodi imfa ni mapeto a zonse?
Lemba: Yobu 14:14, 15
Ulalo: Kodi umoyo udzakhala bwanji Mulungu akadzaukitsa okondedwa athu amene anamwalila?
○○●ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
Funso: Kodi umoyo udzakhala bwanji Mulungu akadzaukitsa okondedwa athu amene anamwalila?
Lemba: Yes. 32:18
Ulalo: Kodi Mulungu adzabweletsa bwanji mtendele padziko lapansi?