LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 February tsa. 4
  • “Mulungu Akuonetsa Cikondi Cake Kwa Ife”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Mulungu Akuonetsa Cikondi Cake Kwa Ife”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Dipo—‘Mphatso Yangwilo’ Yocokela kwa Atate
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
  • Dipo la Yesu—Mphatso ya Mulungu Yopambana Zonse
    Zimene Baibo Imaphunzitsa M’ceni-ceni
  • Dipo Ni Mphatso Ya Mulungu Yopambana Zonse
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
  • Pitilizani Kuyamikila Dipo
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 February tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AROMA 4-6

“Mulungu Akuonetsa Cikondi Cake Kwa Ife”

5:8, 18, 21

Mphatso ya dipo imene Yehova anapeleka, ndiyo maziko othetsela nkhani zikulu-zikulu zokhudza cilengedwe conse, monga ya kuyeletsa dzina lake na kukweza ucifumu wake. Komanso, dipo limathandiza kuti Yehova azitiona kukhala olungama. Linapangitsanso kuti anthu onse omvela akhale na ciyembekezo ca tsogolo labwino.

Kodi tingaonetse bwanji kuti timayamikila mphatso ya dipo?

  • Munthu akubatizika

    Kudzipatulila na kubatizika kumaonetsa kuti timakhulupilila nsembe ya dipo, na kuti tifuna kukhala ku mbali ya Yehova

  • Abale aŵili akulalikila uthenga wabwino wabwino

    Kulalikila uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu kumaonetsa kuti tikutengela citsanzo ca Yehova cokonda anthu amitundu yonse.—Mat. 22:39; Yoh. 3:16

Ni m’njila zinanso ziti zimene ningaonetsele ciyamikilo canga kwa Yehova pa mphatso ya dipo?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani