CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AGALATIYA 1-3
“Ndinamutsutsa Pamasom’pamaso”
2:11-14
Kodi nkhaniyi ionetsa bwanji kuti:
Tifunika kukhala olimba mtima?—w18.03 31-32 ¶16
Kuopa anthu kumachela msampha?—it-2 587 ¶3
Anthu a Yehova kuphatikizapo amene amatitsogolela, ni opanda ungwilo?—w10 6/15 17-18 ¶12
Tifunika kupitiliza kucotsa tsankho m’mitima yathu? —w18.08 9 ¶5