LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 12
  • Yehova Ni Mulungu Woganizila Ena

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Ni Mulungu Woganizila Ena
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • Khalanibe Odzicepetsa Zinthu Zikakuyendelani Bwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Zimene Tingaphunzile kwa Samueli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • “Ndinamutsutsa Pamasom’pamaso”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 12
Zithunzi: 1. Samueli wacicepele akumvetsela pamene Yehova akukamba naye. 2. Samueli akufotokozela Eli uthenga umene Yehova wamuuza.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Ni Mulungu Woganizila Ena

Samueli anaganiza kuti Eli anali kumuitana (1 Sam. 3:4-7; w18.09 24 ¶3)

Yehova anaonetselatu kuti iye ndiye anali kuitana Samueli (1 Sam. 3:8, 9)

Yehova anacita zinthu mom’ganizila Samueli wacicepeleyo (1 Sam. 3:15-18; w18.09 24 ¶4)

DZIFUNSENI KUTI: ‘Ningaonetse bwanji kuti nimawaganizila acicepele komanso acikulile? Ningaonetse bwanji kuti nimaganizila ena pa misonkhano yacikhristu?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani