LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 15
  • “Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Kutumikila Yehova Sikovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Zimene Tingaphunzile pa Mafanizo a m’Nyimbo Youzilidwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Mbili Yanu ili Ngati ya Yobu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 15

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”

Muzimvela Yehova cifukwa comuopa na kum’konda (Deut. 10:12; w09 10/1 10 ¶3-4)

Kumvela kumabweletsa madalitso (Deut. 10:13; w09 10/1 10 ¶6)

Yehova amafuna kuti tikhale bwenzi lake (Deut. 10:15; cl 16 ¶2)

Yehova satikakamiza kuti tizimumvela. Koma amafuna kuti tizimukonda na kumumvela “mocokela pansi pamtima.” (Aroma 6:17) Anthu amene asankha kutumikila Yehova amakhala na umoyo wabwino koposa.

Zithunzi: Mayi asankha kutumikila Yehova. 1. Akumwa moŵa komanso kukoka fodya. 2. Akhudzidwa mtima kwambili na mfundo inayake imene waphunzila pa phunzilo la Baibo. 3. Akambilana mwacimwemwe na mabwenzi ake amene amatumikila Yehova.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani