LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 15
  • Zimene Tingaphunzile pa Mafanizo a m’Nyimbo Youzilidwa

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zimene Tingaphunzile pa Mafanizo a m’Nyimbo Youzilidwa
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Kutumikila Yehova Sikovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • “Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Mukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
  • Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 15

Mose akuphunzitsa anthu a Mulungu nyimbo yolemekeza Yehova

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tingaphunzile pa Mafanizo a m’Nyimbo Youzilidwa

Kaphunzitsidwe kathu kangakhale kotsitsimula ngati mame (Deut. 32:2, 3; w20.06 10 ¶8-9; onani cithunzi pacikuto)

Yehova ni Thanthwe (Deut. 32:4; w09 5/1 14 ¶4)

Yehova amateteza anthu ake monga mmene ciwombankhanga cimatetezela anapiye ake (Deut. 32:11, 12; w01 10/1 9 ¶7)

Zithunzi: Mafanizo opezeka mu Deuteronomo caputala 32. 1. Madontho a mame pa udzu. 2. Thanthwe lalikulu, lokhazikika ngati phili. 3. Ciwombankhanga cikuteteza anapiye ake.

Mungapeze kuti mafanizo abwino oseŵenzetsa pophunzitsa?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani