LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 4
  • Zimene Tingaphunzile pa Kusamvana Kumene Kunacitika

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zimene Tingaphunzile pa Kusamvana Kumene Kunacitika
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Malangizo Othela a Yoswa kwa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Tsatilani Yehova na Mtima Wonse
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kukhala Okhutila Komanso Odzicepetsa?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 4
Aisiraeli okhala ku dela la kum’maŵa kwa mtsinje wa Yorodano akuyankha Aisiraeli anzawo okhala ku dela lina amene akuwanena kuti acita zinthu mosakhulupilika.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zimene Tingaphunzile pa Kusamvana Kumene Kunacitika

Mafuko a Isiraeli okhala kum’maŵa kwa mtsinje wa Yorodano anamanga guwa la nsembe lalikulu zedi (Yos. 22:10)

Mafuko enawo anayamba kuwanena kuti zimene anacitazo n’kusakhulupilika (Yos. 22:12, 15, 16; w06 4/15 5 ¶3)

Mafuko amene ananamizilidwawo anayankha modekha, ndipo izi zinapewetsa nkhondo (Yos. 22:21-30; w08 11/15 18 ¶5)

Kodi nkhaniyi itiphunzitsa kuti tiyenela kucita zinthu motani ngati ena atinamizila kuti tacita colakwa cinacake? Nanga itiphunzitsa ciani za kufunika kopewa kukhulupilila nkhani tisanadziŵe zoona zake?—Miy. 15:1; 18:13.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani