LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsa. 6
  • N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kukhala Okhutila Komanso Odzicepetsa?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kukhala Okhutila Komanso Odzicepetsa?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Zimene Tingacite Kuti Tilandile Madalitso a Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • “Nthawi Yomweyo N’napemphela”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kudzicepetsa N’kwabwino Kuposa Kunyada
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 September tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kukhala Okhutila Komanso Odzicepetsa?

Mneneli wa Mulungu anakana mphatso yaikulu imene Yerobowamu anam’lonjeza (1 Maf. 13:7-10; w08 8/15 8 ¶4)

Pambuyo pake, mneneliyo anaphwanya lamulo la Yehova lomveka bwino (1 Maf. 13:14-19; w08 8/15 11 ¶15)

Kusamvela kwake kunam’bweletsela mavuto (1 Maf. 13:20-22; w08 8/15 9 ¶10)

Makolo akukambilana za ndalama pamene ana awo akuseŵela capafupi.

Ngati ndife okhutila ndipo timapempha citsogozo ca Yehova popanga zisankho, tingapewe mavuto ambili.—1 Tim. 6:8-10.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Ningaonetse bwanji kuti ndine wokhutila na zinthu zofunikila zimene nili nazo? Nanga ningaonetse bwanji kuti ndine wodzicepetsa popanga zisankho?’—Miy. 3:5; 11:2.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani