LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 6
  • “Nthawi Yomweyo N’napemphela”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Nthawi Yomweyo N’napemphela”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Nehemiya Anali Kufuna Kutumikila Ena, Osati Kutumikilidwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mpanda wa Yerusalemu Umangidwanso
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Mpanda Wa Yerusalemu
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kukhala Okhutila Komanso Odzicepetsa?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Nthawi Yomweyo N’napemphela”

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Nehemiya.]

Nehemiya anapemphela asanayankhe funso la mfumu (Neh. 2:2-4; w08 2/15 3 ¶5)

Mfumu inamva pempho la Nehemiya (Neh. 2:5, 6)

Mwaulemu, Mboni yacinyamata ifotokozela aphunzitsi ake zimene imakhulupilila m’kalasi. M’kalasi muli cithunzi coonetsa mbendela ya utawaleza wocilikiza ufulu wa anthu a manthanyula.

ZOYENELA KUSINKHASINKHA: Tingacite ciyani tikauzidwa kuti tifotokoze zimene timakhulupilila nthawi yomweyo popanda kukonzekela?—be 177 ¶4.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani