LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 September tsa. 2
  • Tamandani Yehova Cifukwa ca Nzelu Zake

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tamandani Yehova Cifukwa ca Nzelu Zake
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Anaona Nzelu Kukhala Zofunika Kwambili
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Pemphelo la Solomo Lodzicepetsa Komanso Locokela Pansi pa Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Phindu la Nzelu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Malamulo a Yehova ni Anzelu Komanso Olungama
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 September tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tamandani Yehova Cifukwa ca Nzelu Zake

Yehova anapatsa Solomo nzelu zapadela (1 Maf. 10:1-3; w99 7/1 30 ¶6)

Mfumukazi ya ku Sheba inadabwa na nzelu zimene Yehova anapatsa Solomo (1 Maf. 10:4, 5; w99 11/1 20 ¶6)

Mfumukazi ya ku Sheba inatamanda Yehova cifukwa cosankha Solomo kukhala mfumu (1 Maf. 10:6-9; w99 7/1 30-31)

Mlongo akulalikila mzimayi pa malo odyela.

Mofanana na mfumukazi ya ku Sheba, tiyenela kuonetsa kuti timayamikila nzelu zimene Mulungu amapeleka. Tingaonetse bwanji kuyamikila? Njila imodzi ni kuseŵenzetsa pa umoyo wathu zimene Yesu anaphunzitsa, komanso kuyesetsa kutsatila citsanzo cake. (Mat. 12:42; 1 Pet. 2:21) Njila ina ni kuuzako ena za nzelu zocokela kwa Mulungu pamene tilalikila.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani