LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 14
  • Pemphelo la Solomo Lodzicepetsa Komanso Locokela Pansi pa Mtima

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pemphelo la Solomo Lodzicepetsa Komanso Locokela Pansi pa Mtima
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Tamandani Yehova Cifukwa ca Nzelu Zake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Phindu la Nzelu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Anagwila Nchito Molimbika Cifukwa Cokonda Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Solomo Amanga Kacisi
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 14
Solomo wagwada patsogolo pa guwa lansembe ndipo akupemphela. Kumbuyo kwake kuli anthu.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pemphelo la Solomo Lodzicepetsa Komanso Locokela Pansi pa Mtima

Pa mwambo wotsegulila kacisi, Solomo anapeleka pemphelo locokela pansi pa mtima pamaso pa anthu (1 Maf. 8:22; w09 11/15 9 ¶9-10)

Solomo anatamanda Yehova m’malo modzifunila yekha ulemelelo (1 Maf. 8:23, 24)

Solomo anapemphela na mzimu wodzicepetsa (1 Maf. 8:27; w99 1/15 17 ¶7-8)

Solomo anapeleka citsanzo cabwino, maka-maka kwa amene amapeleka mapemphelo oimilako gulu. Tiziganizila kwambili mmene zokamba zathu zidzamvekela kwa Yehova, kuposa mmene zidzamvekela kwa anthu.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani