LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 10
  • Anaona Nzelu Kukhala Zofunika Kwambili

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Anaona Nzelu Kukhala Zofunika Kwambili
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Tamandani Yehova Cifukwa ca Nzelu Zake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Malamulo a Yehova ni Anzelu Komanso Olungama
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Pemphelo la Solomo Lodzicepetsa Komanso Locokela Pansi pa Mtima
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Munthu Akafa, Kodi Angakhalenso Ndi Moyo?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 10
Mfumukazi ya ku Sheba yabweletsa mphatso kwa Mfumu Solomo. Mfumu Solomo yaimilila kuti ilandile mfumukaziyo. Oimba komanso alonda aimilila m’munsi mwa masitepu opita ku mpando wacifumu wa Solomo.

Mfumukazi ya ku Sheba yafika ku nyumba yacifumu ya Solomo

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Anaona Nzelu Kukhala Zofunika Kwambili

Mfumukazi ya ku Sheba inayenda ulendo wautali komanso wovuta kuti ikaone Solomo (2 Mbiri 9:1, 2; w99 11/1 20 ¶4; w99 7/1 30 ¶4-5)

Itaona nzelu za Solomo na cuma cake, inasoŵa conena (2 Mbiri 9:3, 4; w99 7/1 30-31; onani cithunzi ca pacikuto)

Mfumukaziyo inatamanda Yehova cifukwa ca zimene inaona (2 Mbiri 9:7, 8; it-2 990-991)

Mfumukazi ya ku Sheba na gulu la ngamila zake ikupita kukaona Mfumu Solomo.

Mfumukazi ya ku Sheba inaona kuti nzelu n’zofunika kwambili moti inalolela kutailapo zambili kuti izipeze.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi nimayesetsa kufuna-funa nzelu mmene ningacitile pofuna-funa cuma cobisika?’—Miy. 2:1-6.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani