LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 15
  • Seŵenzetsani Mfundo za m’Baibo Pothandiza Ana Anu Kuti Apambane

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Seŵenzetsani Mfundo za m’Baibo Pothandiza Ana Anu Kuti Apambane
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Zisankho Zimene Zimaonetsa Kuti Timadalila Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kufuna-funa Nzelu mwa Kuŵelenga Baibo Tsiku Lililonse
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Makolo—Phunzitsani Ana Anu Kukondweletsa Mulungu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Muzivomeleza Kuti Pali Zimene Simudziwa
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 15
Zithunzi: Makolo akuphunzitsa mwana wawo pamene akukula. 1. Mayi akuseŵenzetsa buku lakuti “Phunzilani kwa Mphunzitsi Waluso” pophunzitsa mwana wawo wamng’ono. 2. Mwanayo atakulako, atate ake akumuphunzitsa kukonzekela phunzilo la “Nsanja ya Mlonda”. 3. Mwanayo atakula, akulalikila mayi mu ulaliki wa kunyumba na nyumba.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Seŵenzetsani Mfundo za m’Baibo Pothandiza Ana Anu Kuti Apambane

Makolo acikhristu amafuna kuti ana awo akhale na umoyo wacimwemwe komanso wowapindulila potumikila Yehova. Makolo angathandize ana awo kukhala na umoyo wopambana ngati aseŵenzetsa mfundo za m’Baibo powaphunzitsa—Miy. 22:6.

  • Thandizani ana anu kuti azimasuka kukamba nanu.—Yak. 1:19

  • Aphunzitseni mwa citsanzo canu cabwino.—Deut. 6:6

  • Muzicita zinthu zokhudza kulambila nthawi zonse.—Aef. 6:4

ONELELANI VIDIYO YAKUTI MANGANI NYUMBA IMENE IDZAKHALITSA—PHUNZITSANI ANA ANU ‘M’NJILA YOWAYENELELA,’ KENAKO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Kodi makolo angaonetse bwanji kuti saumitsa zinthu?

  • Nanga angaseŵenzetse bwanji mfundo ya pa Yakobo 1:19?

  • N’ciyani cimene makolo angacite pakabuka mavuto?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani