LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 5
  • Mfumu Solomo Anapanga Cisankho Colakwika

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mfumu Solomo Anapanga Cisankho Colakwika
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Muzilimbikitsa Ena pa Nthawi Zovuta
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Kodi Mumapindula Nawo Mofikapo Mawu a Mulungu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Pindulani na Ulangizi Wanzelu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 5
Mfumu Solomo ikuganizila zimene ingacite. Zithunzi: 1. Mzinda wokhala na mpanda wolimba. 2. Mahosi na Magaleta. 3. Amuna aŵili akugwila nchito zolimba pomanga mpanda wamiyala.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mfumu Solomo Anapanga Cisankho Colakwika

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 2 Mbiri.]

Solomo anasonkhanitsa mahosi na magaleta ambili ogulidwa ku Iguputo (Deut. 17:15, 16; 2 Mbiri 1:14, 17)

Mahosi na magaleta amenewo anali kugwilitsidwa nchito na gulu lankhondo la Solomo, ndipo panafunika mizinda yosungilako zinthu zimenezo komanso anthu ambili ozisamalila (2 Mbiri. 1:14; it-1 174 ¶5; 427)

Pa nthawi imene Solomo anali kulamulila bwino, Aisiraeli anali pa ulemelelo. Koma mu ulamulilo wa Mfumu Rehobowamu, iwo anapanduka cifukwa iye anapitiliza kuwasenzetsa goli lolemela la atate ake, komanso anawonjezela kulemela kwake. (2 Mbiri 10:3, 4, 14, 16) Zisankho zathu nthawi zonse zimakhala na zotulukapo zake.—Agal. 6:7.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani