LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 12
  • Pindulani na Ulangizi Wanzelu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pindulani na Ulangizi Wanzelu
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Akanayanjidwa na Mulungu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2018
  • N’cifukwa Ciyani Tiyenela Kufunsila Ulangizi?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
  • “Mtima Wanga Udzakhala Pamenepa Nthawi Zonse”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mfumu Solomo Anapanga Cisankho Colakwika
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pindulani na Ulangizi Wanzelu

Rehobowamu anafunika kupanga cisankho (2 Mbiri 10:1-4; w18.06 13 ¶3)

Rehobowamu anafunsila malangizo (2 Mbiri 10:6-11; w01 9/1 28-29)

Rehobowamu na anthu ake anakumana na mavuto cifukwa iye anakana ulangizi wanzelu (2 Mbiri 10:12-16; it-2 768 ¶1)

Mlongo wacitsikana akumvetsela mosamala pamene mlongo wacikulile akukamba naye pa malo odyela cakudya.

Akhristu acikulile komanso okhwima kuuzimu amadziŵa zambili. Conco, nthawi zambili iwo amadziŵa zotulukapo za cisankho cimene munthu angapange.—Yobu 12:12.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Ndani mumpingo mwathu amene anganipatse ulangizi wabwino?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani