LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 15
  • Tengelani Cikondi Cosasintha ca Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tengelani Cikondi Cosasintha ca Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Cikondi Cosasintha ca Yehova N’ciani?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Cikondi Cokhulupilika Cimam’kondweletsa Yehova—Nanga Imwe?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
  • Cikondi ca Mulungu Cokhulupilika Cidzakhalapo Mpaka Kale-kale
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
  • Yehova Amakukonda Kwambili
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 15

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Tengelani Cikondi Cosasintha ca Yehova

Yehova ndiye citsanzo cabwino kwambili pa nkhani yoonetsa cikondi cosasintha. (Sal. 103:11) Ici si cikondi ca kanthawi cabe. Cikondi cosasintha ni cikondi cacikulu komanso cokhalitsa. Yehova anaonetsa khalidwe limeneli kwa anthu ake Aisiraeli m’njila zambili. Anawamasula mu ukapolo ku Iguputo na kuwaloŵetsa m’Dziko Lolonjezedwa. (Sal. 105:42-44) Anali kuwamenyela nkhondo, ndipo mobweleza-bweleza anawakhululukila macimo awo. (Sal. 107:19, 20) ‘Tikamacita cidwi na nchito za Yehova’ zoonetsa cikondi cake cosasintha, timalimbikitsidwa kutengela citsanzo cake.—Sal. 107:43.

Zithunzi: Zithunzi zozikika pa vidiyo yakuti “Ganizilani Nchito za Yehova Zoonetsa Cikondi Cake Cokhulupilika.” 1. M’bale Capra na m’bale wina apita kukacezela mlongo kunyumba kwake. 2. M’bale Capra, amene tsopano ali m’ndende pamodzi na abale ena, akupatsa cakudya m’bale wina wodwala amene wagona pabedi.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI “GANIZILANI NCHITO ZA YEHOVA ZOONETSA CIKONDI CAKE COKHULUPILIKA,” NDIYENO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Kodi tingaonetse cikondi cosasintha m’njila ziti?

  • N’cifukwa ciyani kuonetsa cikondi cosasintha kumafuna kudzimana?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani