LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 3
  • Thandizani Ena Kucita Zonse Zimene Angathe Potumikila Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Thandizani Ena Kucita Zonse Zimene Angathe Potumikila Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Anagwilitsa Nchito Udindo Wake Pothandiza Ena
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Citsanzo Cimene Tingatengele pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Yesetsani Kukhala Wodzicepetsa Monga Esitere
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 3

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Thandizani Ena Kucita Zonse Zimene Angathe Potumikila Yehova

Moredekai anapeleka citsanzo cabwino pa nkhani yokhala wolimba mtima komanso wokhulupilika kwa Yehova (Esitere 3:​2-4; it-2 431 ¶7)

Iye anathandiza Esitere kuona zimene akanacita pothandiza anthu ake (Esitere 4:​7, 8; it-2 431 ¶9)

Analimbikitsa Esitere kukhala wolimba mtima na kudalila Yehova (Esitere 4:​12-14; ia 133 ¶22-23)

Zithunzi: 1. Mkulu akulimbikitsa m’bale wacinyamata mu ulaliki. 2. M’bale wacinyamata akulemba fomu yofunsila kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu. 3. Pambuyo pake, m’baleyo watsiliza Sukulu ya Alengezi a Ufumu.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zocita na zokamba zanga zimalimbikitsa ena mumpingo kucita zonse zimene angathe potumikila Yehova?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani