LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w23 October tsa. 32
  • Mfundo Yothandiza pa Kuŵelenga Kwanu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mfundo Yothandiza pa Kuŵelenga Kwanu
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Mungapezele Masinthidwe pa Kamvedwe Kathu Katsopano
  • Mfundo Yothandiza Pofufuza
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Mfundo Yothandiza Pa Kuŵelenga Kwanu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Cida Catsopano Cofufuzila
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Kodi Tingapindule Bwanji ndi Laibulale ya pa Nyumba ya Ufumu?
    Ndani Amene Akucita Cifunilo Ca Yehova Masiku Ano?
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
w23 October tsa. 32

Mfundo Yothandiza pa Kuŵelenga Kwanu

Mmene Mungapezele Masinthidwe pa Kamvedwe Kathu Katsopano

Ni mwayi wapadela kukhala m’nthawi imene Yehova akumveketsa bwino coonadi ca m’Baibo kuposa n’kale lonse. (Dan. 12:⁠4) Ngakhale n’telo, zingakhalebe zovuta kwa ife kuti tiziyendela pamodzi na kamvedwe katsopano ka m’Baibo. Kodi tingapeze kuti kamvedwe katsopano kameneka na kafotokozedwe kake?

• Mu Watch Tower Publications Index pansi pa ka mutu kakuti “Beliefs Clarified” pamafotokoza kamvedwe katsopano motsatila caka. Kuti mupeza nkhanizo, lembani mawu akuti “understanding clarified” m’danga lofufuzila la pa Watchtower Library kapena pa Laibulale ya pa Intaneti ya Watchtower™

• Buku Lofufuzila la Mboni za Yehova ili na nkhani zocepa, ndipo imazindandalika motsatila mitu yake. Pitani pa kamutu kakuti “Mboni za Yehova,” kenako “Zikhulupililo za Akhristu na Mmene Amaonela Nkhani Zina,” ndiyeno pitani pa kamutu kakuti “Kamvedwe Katsopano ka Zimene Timakhulupilila.”

Pa phunzilo la inu mwini, mungasankhe nkhani ya kamvedwe kathu katsopano ya posacedwa. Fufuzani pamene panasintha na kuona zifukwa za m’Malemba zimene zinacititsa kuti pakhale kusinthako.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani