February Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano February 2018 Makambilano a Citsanzo February 5-11 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 12-13 Fanizo la Tiligu ndi Namsongole UMOYO WATHU WACIKHRISTU Mafanizo a Ufumu na Tanthauzo Lake Kwa Ise February 12-18 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 14-15 Kudyetsa Anthu Ambili Mwa Kugwilitsila Nchito Anthu Ocepa UMOYO WATHU WACIKHRISTU Uzilemekeza Atate Ako ndi Amayi Ako February 19-25 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 16-17 Kodi Muli na Maganizo a Ndani? UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuseŵenzetsa Mafunso Mwaluso February 26–March 4 CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MATEYU 18-19 Muzisamala Kuti Musadzipunthwitse Kapena Kupunthwitsa Ena