LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 151
  • Adzaitana

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Adzaitana
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Iye Adzaitana
    Imbirani Yehova
  • Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha
    Imbirani Yehova
  • Lonjezo la Moyo Wamuyaya
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Khulupilila Coonadi Iwe Mwini
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 151

NYIMBO 151

Adzaitana

Yopulinta

(Yobu 14:13-15)

  1. 1. Moyo wathu uli ngati mame,

    Amene sakhalitsa.

    Mwacisoni ‘se timamwalila,

    Ena ‘tsala alila.

    Koma Mulungu analonjeza,

    Akufa adzauka.

    (KOLASI)

    Yehova adzaitana;

    Akufa adzayankha,

    Ndipo adzakhaladi

    Na moyo wamuyaya.

    Conco tisakaikile

    Lonjezo lake M’lungu.

    Iye sangaiŵale

    Nchito ya manja ake.

  2. 2. Atumiki a Yehova M’lungu

    Ngakhale atisiye,

    M’lungu wathu adzaŵaukitsa,

    Ndipo adzaŵapatsa

    Moyo wosatha m’paradaiso

    M’dziko lopanda imfa.

    (KOLASI)

    Yehova adzaitana;

    Akufa adzayankha,

    Ndipo adzakhaladi

    Na moyo wamuyaya.

    Conco tisakaikile

    Lonjezo lake M’lungu.

    Iye sangaiŵale

    Nchito ya manja ake.

(Onaninso Yoh. 6:40; 11:11, 43; Yak. 4:14.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani