LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 51
  • Timamatire Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Timamatire Yehova
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova, Mulungu Wamkulu
    Imbirani Yehova
  • Mulungu Wamkulu, Yehova
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Ufumu wa Yehova Wayamba Kulamulira
    Imbirani Yehova
  • Ulamulilo wa Yehova Wayamba
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Imbirani Yehova
sn nyimbo 51

Nyimbo 51

Timamatire Yehova

(Yoswa 23:8)

1. Yehova ndi woyenera kulamulira.

Amachita zinthu zonse mwachilungamo.

Zonse zomwe wanena zimachitika.

Timumamatire, timuyandikire;

Ufumu wake ndi wopindulitsa.

2. Ulamuliro wake ndi wachilungamo.

Pokhala pakenso ndi paulemerero.

Iye aitana ofatsa abwere.

Timamatire M’lungu ndi wopambana;

Woyenera kuti tizimulambira.

3. M’mwamba ndi mosakwana kuti akhalemo.

Palibe wolepheretsa zofuna zake.

Adzakwaniritsa zomwe walonjeza.

Timumamatire, timutumikire,

Tikhale odziperekadi kwa iye.

(Onaninso Deut. 4:4; 30:20; 2 Maf. 18:6; Sal. 89:14.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani