LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 38
  • Umutulire Yehova Nkhawa Zako

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Umutulire Yehova Nkhawa Zako
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Tulila Yehova Nkhawa Zako
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Mvelani Pemphelo Langa Conde
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Mulungu Imvani Pemphero Langa
    Imbirani Yehova
  • Thawirani ku Ufumu wa Mulungu
    Imbirani Yehova
Onaninso Zina
Imbirani Yehova
sn nyimbo 38

Nyimbo 38

Umutulire Yehova Nkhawa Zako

(Salmo 55)

1. Chonde, ndimveni Yehova,

Musandinyalanyaze.

Mundiyankhe pempho langa,

Mundichotsere mantha.

(KOLASI)

Tulira Yehova nkhawa

Ndipo adzakuchirikiza.

Iye sadzalola kuti

Ugwedezeke konse.

2. N’kadakhala ndi mapiko,

Ndikanaulukadi,

Kuti ofuna kundipha,

Asandipeze konse.

(KOLASI)

Tulira Yehova nkhawa

Ndipo adzakuchirikiza.

Iye sadzalola kuti

Ugwedezeke konse.

3. Ndidzafu’lira Yehova

Kuti anditeteze.

Iye apatsa mtendere Kwa

atumiki ake.

(KOLASI)

Tulira Yehova nkhawa

Ndipo adzakuchirikiza.

Iye sadzalola kuti

Ugwedezeke konse.

(Onaninso Sal. 22:5; 31:2-24.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani