CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 PETULO 1-3
‘Muzikumbukila Nthawi Zonse Kubwela Kwa Tsiku la Yehova’
3:11, 12
Yehova sadzazengeleza kuweluza anthu mwacilungamo pa nthawi yake. Kodi zocita zathu zimaonetsa kuti talikonzekela tsiku la Yehova?
Kodi kukhala na ‘khalidwe loyela ndiponso kucita nchito zosonyeza kuti ndinu odzipeleka kwa Mulungu’ kutanthauza ciani?
Tifunika kukhala oyela m’makhalidwe athu ndiponso kuteteza cikhulupililo cathu
Nthawi zonse tiyenela kucita zinthu mogwilizana na kulambila kwathu, kaya pagulu kapena kwatokha