October 28–November 3
2 PETULO 1-3
Nyimbo 114 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Muzikumbukila Nthawi Zonse Kubwela Kwa Tsiku la Yehova”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 2 Petulo.]
2 Pet. 3:9, 10—Tsiku la Yehova lidzafika pa nthawi yake (w06 12/15 27 ¶11)
2 Pet. 3:11, 12—Tiyenela kuganizila za mtundu wa munthu amene tifunika kukhala (w06 12/15 19 ¶18)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
2 Pet. 1:19—Kodi “nthanda” ikuimila ndani ndipo iyeyo anatuluka liti? Nanga tidziŵa bwanji kuti zimenezi zinacitika kale? (w08 11/15 22 ¶2)
2 Pet. 2:4—Kodi “Tatalasi” n’ciani ndipo angelo opanduka anaponyedwamo liti? (w08 11/15 22 ¶3)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 2 Pet. 1:1-15 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Waciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 7)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) bhs 154-155 ¶3-4 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kodi Mumawakonda Kwambili Mawu A Mulungu?”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti, Anailemekeza Kwambili Baibo—Kambali kake (William Tyndale)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 88 ¶12-19
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 49 na Pemphelo