LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 63
  • Ndise Mboni za Yehova!

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ndise Mboni za Yehova!
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Ndife Mboni za Yehova!
    Imbirani Yehova
  • Cuma Capadela
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Cuma Capadela
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Dzina Lanu Ndimwe Yehova
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 63

NYIMBO 63

Ndise Mboni za Yehova!

Yopulinta

(Yesaya 43:10-12)

  1. 1. Anthu amalambila,

    Milungu ya mitengo.

    Mulungu woona

    Iwo sam’dziŵa.

    M’lungu Wamphamvuzonse

    Ni Atate Yehova.

    Milungu ina ni yabodza,

    Ilibiletu na mboni.

    (KOLASI)

    Mboni’fe za Yehova,

    Sitimayopa anthu.

    Wathu ni M’lungu wa ulosi;

    Amakamba zoona.

  2. 2. Ise timalengeza

    Dzina la M’lungu wathu.

    Timalalikila

    Molimba mtima.

    Ticitila umboni

    Za Ufumu wa M’lungu.

    Ndipo timathandiza ena,

    Kumutamanda Yehova.

    (KOLASI)

    Mboni’fe za Yehova,

    Sitimayopa anthu.

    Wathu ni M’lungu wa ulosi;

    Amakamba zoona.

  3. 3. Dzina la M’lungu wathu,

    Ise timalikweza.

    Timacenjezanso,

    Oipa onse.

    Tiŵauza alape,

    Abwele kwa Mulungu.

    Kudzipeleka kubweletsa

    Madalitso amuyaya.

    (KOLASI)

    Mboni’fe za Yehova,

    Sitimayopa anthu.

    Wathu ni M’lungu wa ulosi;

    Amakamba zoona.

(Onaninso Yes. 37:19; 55:11; Ezek. 3:19.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani