LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 January tsa. 8
  • Mmene Tingatsogozele Phunzilo m’Kabuku ka Uthenga Wabwino

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mmene Tingatsogozele Phunzilo m’Kabuku ka Uthenga Wabwino
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Kugwilitsila Nchito Kabuku ka Uthenga Wabwino Pophunzitsa
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Mmene Tingagwilitsile Nchito Kabuku Kakuti Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu!
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuonetsa Mocitila Phunzilo la Baibulo Pogwilitsila Nchito Buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
  • Gwilitsilani Nchito Webusaiti ya jw.org mu Utumiki
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 January tsa. 8

KUONJEZELA LUSO LANU MU ULALIKI

Mmene Tingatsogozele Phunzilo m’Kabuku ka Uthenga Wabwino

  1. Ŵelengani funso lili m’zilembo zakuda lokhala ndi nambala kuti muthandize mwininyumba kumvetsa mfundo yaikulu.

  2. Ŵelengani ndime ili munsi mwa funsolo.

  3. Ŵelengani malemba olembedwa mopendeketsa, ndipo funsani mafunso mwaluso kuti muthandize mwininyumba kuzindikila mmene malembawo akuyankhila funsolo.

  4. Ngati pali ndime ina munsi mwa funso limenelo, tsatilaninso malangizo amene alembedwa pa 2 ndi 3 pamwambapa. Ngati pa jw.org pali vidiyo yogwilizana ndi funsolo, mungaonetse mwininyumba vidiyoyo mkati mwa phunzilo lanu.

  5. Pofuna kutsimikizila kuti mwininyumba wamvetsetsa mfundo imene mwakambilana, mufunseninso funso lili m’zilembo zakuda.

Phunzilo 2 m’kabuku ka Uthenga Wabwino Wocokela kwa Mulungu
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani