LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 5
  • Zacilengedwe Zimatilimbikitsa Kudalila Kwambili Nzelu za Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zacilengedwe Zimatilimbikitsa Kudalila Kwambili Nzelu za Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Acinyamata—Auzeni za Mumtima Mwanu Makolo Anu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 5
Zithunzi: 1. Nyelele zondondozana zanyamula masamba. 2. Njuci ikuuluka pafupi na duwa.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Zacilengedwe Zimatilimbikitsa Kudalila Kwambili Nzelu za Yehova

Kodi nthawi zonse Yehova amadziŵa zimene zili zabwino kwambili kwa ife? Inde! Popeza timakhulupilila zimenezi, timaonetsa nzelu mwa kumvela malangizo ake. (Miy. 16:3, 9) Koma nthawi zina, tingayambe kukayikila citsogozo ca Yehova ngati malangizo ake asiyana na maganizo athu. N’ciani cimene tingacite kuti tizidalila kwambili nzelu za Yehova? Tiyenela kusinkhasinkha pa zimene iye analenga.—Miy. 30:24, 25; Aroma 1: 20.

ONELELANI VIDIYO YAKUTI KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA? MMENE NYERERE ZIMAPEWERA KUTCHINGILANA NJIRA, NDIYENO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Kodi nyelele zambili zimacita ciani tsiku lililonse?

  • Kodi nyelele zimapewa bwanji kuchingilana njila?

  • Kodi anthu angaphunzile ciani pa kayendedwe ka nyelele?

ONELELANI VIDIYO YAKUTI KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA? MMENE NJUCHI IMAULUKIRA, NDIYENO YANKHANI MAFUNSO AWA:

  • Ni mavuto otani amene anthu oyendetsa ndeke zing’ono-zing’ono amakumana nawo?

  • Kodi njuci zing’ono-zing’ono za mtundu winawake zimakwanitsa bwanji kuuluka bwino-bwino osatengeka na mphepo?

  • Kodi anthu kutsogoloku afuna kukapanga ciani potengela nzelu zacibadwa za mtundu wa njuci zimenezi?

Kodi mwaona umboni wotani wa nzelu za Yehova pa zacilengedwe za kwanuko?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani