LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w16 December tsa. 32
  • Mlongoza Nkhani wa Nsanja ya Mlonda 2016

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mlongoza Nkhani wa Nsanja ya Mlonda 2016
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2016
w16 December tsa. 32

Mlongoza Nkhani wa Nsanja ya Mlonda 2016

Taonetsa kope yake imene mwacokela nkhaniyo

BAIBO

  • Macaputa na Mavesi, Na. 2

  • Lefèvre d’Étaples (womasulila), Na. 6

  • Mmene Yapulumukila, Na. 4

BAIBO IMASINTHA ANTHU

  • Zinanitengela Nthawi Yaitali (J. Mutke), Na. 4

  • Ndinaphunzila Kulemekeza Akazi (J. Ehrenbogen), Na. 3

  • N’nali Woipa Mtima Kwambili ndi Waciwawa (A. De la Fuente), Na. 5

  • UMOYO NA MAKHALIDWE ACIKHIRISTU

Kuposa Golide (nzelu yaumulungu), Aug.

  • Kuteteza Uthenga Wabwino Pamaso pa a Boma, Sept.

  • Mungathandize Ena Mumpingo Wanu, Mar.

  • Pitilizani Kutumikila Yehova Mwacimwemwe, Feb.

  • Kufatsa—Kumaonetsa Nzelu, Dec.

  • Labwino Kwambili Kuposa Dayamondi (kuona mtima), June

  • ‘Nzelu Zopindulitsa,’ Oct.

  • Tuakacisi Topatulika Kukalambila? Na. 2

  • Utumiki Wanu Uli Ngati Mame? Apr.

  • YEHOVA

  • “Usacite Mantha. Ndikuthandiza,” July

  • Dzina, Na. 3

  • MBONI ZA YEHOVA

  • Ubwino Wotsatila Malangizo a Yehova (zocitika mu utumiki), Sept.

  • “Ofalitsa Ufumu ku Britain—Galamukani!” (1937), Nov.

Anadzipeleka ku Ghana, July

  • “Nikolola Zipatso ndi Kutamanda Yehova” (Germany, nkhondo yoyamba ya dziko lonse), Aug.

  • “Nchitoyi Ndi Yaikulu” (zopeleka), Nov.

  • YESU KHIRISTU

Cinthu Cacilendo Cimene Yesu Anacitila Anthu Akhate, Na. 4

  • Atate Ake a Yosefe, Na. 3

  • N’cifukwa Ciani Anavutika Ndi Kufa? Na. 2

  • MBILI YANGA

  • Nakhala Zinthu Zonse Kwa Anthu Osiyana-siyana (D. Hopkinson), Dec.

  • N’nalandila Coonadi Olo Kuti Nilibe Manja (B. Merten), Na. 6

  • Kusiilana Citsanzo Cabwino (T. McLain), Oct.

  • Napeza Cimwemwe Cifukwa Copatsa (R. Parkin), Aug.

  • Yehova Wandidalitsa (C. Robison), Feb.

Masisitele Anakhala Paubale Weniweni Wakuuzimu (F. na A. Fernández), Apr.

  • NKHANI ZOSIYANA-SIYANA

  • “Yehova Ndiye Mwini Nkhondo” (Davide), Na. 5

  • Kodi N’zoona Kuti Davide Anamenyana Ndi Goliyati? Na. 5

Ufulu Umene Aroma Anapatsa Olamulila Aciyuda ku Yudeya, Oct.

  • Mulungu Amayankha Mapemphelo Onse? Na. 6

  • Mfundo Zimene Atsogoleli Acipembedzo Aciyuda Anali Kutsatila Pofuna Kuthetsa Cikwati, Na. 4

  • Kumvela Cenjezo, Na. 2

  • “Inde Ndipita” (Rabeka), Na. 3

  • Phunzilani ku Mbalame, Na. 6

  • Kuyelekezela Zinthu Kopindulitsa Kwambili (zikhulupililo na Baibo), Na. 4

Kukhala m’Cipembedzo Kuli Ndi Phindu? Na. 4

  • Tifunika Kukhala Bwanji Popemphela? Na. 6

  • Anayambitsa Cipembedzo ni Anthu? Na. 4

  • M’nthawi za Baibulo Kunali Nsalu za Mitundu, Na. 3

  • Masomphenya Oonetsa Amene Ali Kumwamba, Na. 6

  • Kodi Ufumu wa Mulungu N’ciani? Na. 5

  • Munthu Amene Mumakonda Akamwalila, Na. 3

  • Kodi Tingapeze Kuti Citonthozo? Na. 5

  • Kodi Mdyelekezi Ndani? Na. 2

  • Mau Amene Anali Atanthauzo Kwambili (“mwanawe”), Nov.

  • Kodi Zidzatheka Kukhala M’dziko Lopanda Nkhanza? Na. 4

  • Kodi N’zoona Kuti Anthu Anali Kubyala Namsongole m’Munda? Oct.

  • MAFUNSO OCOKELA KWA AŴELENGI

  • Ndodo ziŵili zimene zinakhala ndodo imodzi (Ezek. 37), July

  • Mwamuna ndi kacikwama ka mlembi konyamulilamo inki ndi zolembela ndiponso amuna 6 onyamula zida (Ezek. 9:2), June

  • Satana anatenga Yesu mwacindunji ndi kupita naye ku kacisi? (Mat. 4:5; Luka 4:9), Mar.

  • Kodi “mau a Mulungu” n’ciani? (Aheb. 4:12), Sept.

  • Ndi liti pamene anthu a Mulungu anakhala akapolo a Babulo Wamkulu? Mar.

  • Nkhani yosamba m’manja (Maliko 7:5), Aug.

  • NKHANI ZOPHUNZILA

  • Yehova Amatiumba, June

  • Muzilimbikitsidwa ndi Mphatso ya Mulungu Yosatheka Kuifotokoza, Jan.

  • ‘Pitilizani Kukonda Abale’ Jan.

  • Mulungu Amakonda Anthu Okhulupilika, Apr.

  • Pindulani Mokwanila ndi Cakudya Cakuuzimu Cimene Yehova Amapeleka, May

Tinamasulidwa mwa Cisomo ca Mulungu, Dec.

  • Kuitaniwa Kucoka mu Mdima, Nov.

  • Kodi Mavalidwe Anu Amalemekeza Mulungu? Sept.

  • “Musaiŵale Kuceleza Alendo,” Oct.

  • Musakhumudwe ndi Zolakwa za Ena, June

  • “Manja Anu Asakhale Olefuka,” Sept.

  • Kodi Mumalemekeza Buku Lake la Yehova? Nov.

  • Kodi Mumalola Kuti Woumba Wamkulu Akuumbeni? June

  • Kodi Mumaona Kufunika Kopita Patsogolo Kuuzimu? Aug.

  • Kodi Mumaona Kufunika Kophunzitsa Ena? Aug.

  • Khalani na Cikhulupililo m’Malonjezo a Yehova, Oct.

“Pitani Mukaphunzitse Anthu a Mitundu,” May

  • Tiziyamikila Kukoma Mtima Kwakukulu Kumene Tinalandila, July

  • Kodi Mumasankha Bwanji Zocita? May

  • Tengelani Citsanzo ca Mabwenzi Apamtima a Yehova, Feb.

  • Kodi Baibulo Likusinthabe Umoyo Wanu? May

  • Yehova Anamucha kuti “Bwenzi Langa,” Feb.

  • Yehova Amatsogolela Anthu Ake m’Njila ya ku Moyo, Mar.

  • “Yehova Mulungu Wathu Ndi Yehova Mmodzi,” June

  • Yehova Amapeleka Mphoto kwa Anthu Omufuna-funa na Mtima Wonse, Dec.

  • Cilimikani pa Kulimbana Kuti Mupeze Madalitso a Yehova, Sept.

  • ‘Pitilizani Kulimbikitsana Tsiku na Tsiku,’ Nov.

  • Tengelani Citsanzo ca Atumiki Okhulupilika a Yehova, Feb.

  • “Mulole Kuti Kupilila Kumalize Kugwila Nchito Yake,” Apr.

  • Pewani Kutenga Mbali m’Ndale za Dziko Loipali, Apr.

  • Khalanibe Auzimu Potumikila Mumpingo wa Cinenelo Cina, Oct.

  • Kupangitsa Cikwati Cacikhiristu Kukhala Cacimwemwe, Aug.

  • Cikwati—Ciyambi na Cifuno Cake, Aug.

  • Gulu Lake Ladongosolo Monga mwa Buku la Mau Ake, Nov.

  • Makolo, Thandizani Ana Anu Kukhala na Cikhulupililo, Sept.

  • Khalani Wokhulupilika kwa Yehova, Feb.

  • Muzifuna-funa Ufumu, Osati Zinthu Zakuthupi, July

  • ‘Kuika Maganizo Athu pa Zinthu za Mzimu Kumabweletsa Moyo na Mtendele,’ Dec.

  • Tizithetsa Mikangano Mwamtendele, May

  • Lalikilani Uthenga Wabwino Wokamba za Kukoma Mtima, July

  • Limbitsani Cikhulupililo Canu pa Zimene Muyembekezela, Oct.

  • Mzimu Umacitila Umboni Limodzi ndi Mzimu Wathu, Jan.

  • Anamasuka Kucoka ku Cipembedzo Conama, Nov.

  • Tulilani Yehova Nkhawa Zanu Zonse, Dec.

  • “Tipita Nanu Limodzi,” Jan.

  • N’cifukwa Ciani Tiyenela ‘Kukhalabe Maso’? July

  • N’cifukwa Ciani Tiyenela Kusonkhana? Apr.

  • Kugwila Nchito ndi Mulungu—Kumabweletsa Cimwemwe, Jan.

  • Kodi Tingalimbitse Bwanji Mgwilizano Pakati Pathu? Mar.

  • Acinyamata—Kodi Ndinu Okonzeka Kubatizidwa? Mar.

  • Acinyamata—Kodi Mungakonzekele Bwanji Ubatizo? Mar.

  • Wacicepele, Limbitsa Cikhulupililo Cako, Sept.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani