LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • w23 September tsa. 32
  • Mfundo Yothandiza pa Kufufuza Kwanu

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mfundo Yothandiza pa Kufufuza Kwanu
  • Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Zida Zophunzitsila Ana
  • Gwilitsilani Nchito Webusaiti ya jw.org mu Ulaliki—“Khala Bwenzi la Yehova”
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2015
  • Njila Zocitila Kulambila kwa Pabanja
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Pezani Nzelu Zothandiza pa Umoyo pa JW.ORG
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Kulemekezana m’Banja
    Galamuka!—2024
Onaninso Zina
Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2023
w23 September tsa. 32

Mfundo Yothandiza pa Kufufuza Kwanu

Zida Zophunzitsila Ana

Makolo ali na udindo waukulu wophunzitsa ana awo za Yehova. (Aef. 6:4) Pofuna kuwathandiza, gulu la Yehova lafalitsa zida zambili. Kodi mungaziseŵenzetse motani pophunzitsa ana anu?

  • Pitani pa JW.ORG. pamenepo, mudzapezapo zofalitsa zonse zimene anakonzela ana, kuphatikizapo mavidiyo, na nkhani zoŵelenga.a Kuti muzipeze, lembani mau akuti “Ana” kapena “Acinyamata” m’danga lofufuzila.

  • Sankhani zothandiza. Pansi pa kamutu kakuti “Ana,” mungasankhe nkhani, mavidiyo na nyimbo zimene muona kuti n’zothandiza kwambili kwa ana anu. Kuti muzipeze, lembani mau akuti “Zochita pa Kulambila kwa Pabanja” m’danga lofufuzila ku Chichewa.

  • Kambilanani nawo. Pewani kuseŵenzetsa mavidiyo, kapena nkhani zoŵelenga monga zinthu zotangwanitsila mwana wanu akasoŵa zocita. Koma kambilanani naye nkhanizo, na kum’thandiza kukhala pa ubale wolimba na Yehova.

a Palipano, JW Library® ili na mavidiyo ambili a ana m’Cinyanja, koma ili na nkhani zoŵelenga zocepa cabe.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani