Numeri 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndi amene anasankhidwa pa gulu la anthuwo. Iwo anali atsogoleri+ a mafuko a makolo awo, atsogoleri a anthu masauzande mu Isiraeli.”+
16 Amenewa ndi amene anasankhidwa pa gulu la anthuwo. Iwo anali atsogoleri+ a mafuko a makolo awo, atsogoleri a anthu masauzande mu Isiraeli.”+