-
Levitiko 27:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Koma ngati ndi nyama yodetsedwa ndipo waiwombola mogwirizana ndi mtengo womwe unaikidwa, azipereka mtengo wa nyamayo nʼkuwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a mtengowo.+ Koma ngati sangaiwombole izigulitsidwa pa mtengo womwe unaikidwa.
-