-
Deuteronomo 20:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 “Mukapita kunkhondo kukamenyana ndi adani anu, nʼkuona kuti ali ndi mahatchi, magaleta ankhondo komanso asilikali ochuluka kuposa inu, musachite nawo mantha chifukwa Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ali ndi inu.+
-
-
Salimo 18:37, 38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Ndidzathamangitsa adani anga nʼkuwapeza,
Sindidzabwerera mpaka onse nditawawononga.
38 Ndidzawaphwanya kuti asadzukenso.+
Ndidzawapondaponda ndi mapazi anga.
-