-
1 Samueli 19:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Patapita nthawi, nkhondo inayambanso ndipo Davide anapita kukamenyana ndi Afilisiti. Iye anapha Afilisiti ambiri ndipo Afilisiti otsala anagonja nʼkuthawa.
-
-
2 Samueli 10:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma Asiriyawo anayamba kuthawa Isiraeli ndipo Davide anapha asilikali a Siriya 700 okwera magaleta komanso asilikali 40,000 okwera pamahatchi. Iye anaphanso Sobaki, mtsogoleri wa gulu lankhondo la Siriya.+
-